Aroma 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Izi zikutanthauza kuti si ana akuthupi amene alidi ana a Mulungu,+ koma ana obadwa mogwirizana ndi lonjezo+ ndi amene amatengedwa kuti ndi mbadwa.*
8 Izi zikutanthauza kuti si ana akuthupi amene alidi ana a Mulungu,+ koma ana obadwa mogwirizana ndi lonjezo+ ndi amene amatengedwa kuti ndi mbadwa.*