Aroma 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa iye anauza Mose kuti: “Amene ndikufuna kumukomera mtima ndidzamukomera mtima, ndipo amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo.”+
15 Chifukwa iye anauza Mose kuti: “Amene ndikufuna kumukomera mtima ndidzamukomera mtima, ndipo amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo.”+