Aroma 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndi zofanananso ndi zimene ananena mʼbuku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatchula kuti ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sankakondedwa ndidzamutchula kuti ‘wokondedwa.’+
25 Ndi zofanananso ndi zimene ananena mʼbuku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatchula kuti ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sankakondedwa ndidzamutchula kuti ‘wokondedwa.’+