Aroma 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiye pamenepa tinene kuti chiyani? Ngakhale kuti anthu a mitundu ina sanatsatire chilungamo,+ iwo anapeza chilungamo chimene chimabwera chifukwa cha chikhulupiriro.+
30 Ndiye pamenepa tinene kuti chiyani? Ngakhale kuti anthu a mitundu ina sanatsatire chilungamo,+ iwo anapeza chilungamo chimene chimabwera chifukwa cha chikhulupiriro.+