Aroma 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pajatu Mose analemba zokhudza mmene munthu angachitire chilungamo mogwirizana ndi Chilamulo, anati: “Aliyense amene akuchita zimenezi adzakhala ndi moyo chifukwa cha malamulo.”+
5 Pajatu Mose analemba zokhudza mmene munthu angachitire chilungamo mogwirizana ndi Chilamulo, anati: “Aliyense amene akuchita zimenezi adzakhala ndi moyo chifukwa cha malamulo.”+