Aroma 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma za chilungamo chimene chimabwera chifukwa cha chikhulupiriro, Malemba amati: “Mumtima mwako usanene kuti,+ ‘Kodi ndani adzapite kumwamba?’+ kuti akatsitse Khristu.
6 Koma za chilungamo chimene chimabwera chifukwa cha chikhulupiriro, Malemba amati: “Mumtima mwako usanene kuti,+ ‘Kodi ndani adzapite kumwamba?’+ kuti akatsitse Khristu.