-
Aroma 10:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Komabe, kodi angaitane bwanji pa dzina lake ngati samukhulupirira? Angakhulupirire bwanji ngati sanamvepo za iye? Nanga angamve bwanji za iye popanda wina kulalikira?
-