-
Aroma 13:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Choncho amene akutsutsana ndi ulamuliro, akutsutsana ndi zimene Mulungu anakonza. Amene akutsutsana ndi zimene Mulungu anakonza adzalandira chiweruzo.
-