Aroma 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa, osati ngati ukuchita zabwino.+ Choncho kodi ukufuna kuti usamaope olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Nsanja ya Olonda,8/15/1991, tsa. 1911/1/1990, ptsa. 19-20
3 Chifukwa olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa, osati ngati ukuchita zabwino.+ Choncho kodi ukufuna kuti usamaope olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda.