Aroma 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi sichilimbikitsa munthu kuchitira mnzake zoipa,+ choncho chikondi chimathandiza munthu kuti akwaniritse lamulo.+
10 Chikondi sichilimbikitsa munthu kuchitira mnzake zoipa,+ choncho chikondi chimathandiza munthu kuti akwaniritse lamulo.+