Aroma 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikuperekanso moni ku mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwawo.+ Moni kwa wokondedwa wanga Epeneto, amene ndi chipatso choyambirira cha Khristu ku Asia. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:5 Nsanja ya Olonda,11/15/2002, tsa. 710/1/1988, tsa. 13
5 Ndikuperekanso moni ku mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwawo.+ Moni kwa wokondedwa wanga Epeneto, amene ndi chipatso choyambirira cha Khristu ku Asia.