Aroma 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ komanso akaidi anzanga. Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ineyo. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 13
7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ komanso akaidi anzanga. Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ineyo.