-
Aroma 16:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Moni kwa Turufena ndi Turufosa, azimayi ogwira ntchito mwakhama potumikira Ambuye. Moni kwa Peresida, wokondedwa wathu. Mayi ameneyu wagwira ntchito mwakhama potumikira Ambuye.
-