Aroma 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano ndikukulimbikitsani abale, kuti musamale ndi amene amagawanitsa anthu ndiponso kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi zimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:17 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, tsa. 1610/1/1988, tsa. 14
17 Tsopano ndikukulimbikitsani abale, kuti musamale ndi amene amagawanitsa anthu ndiponso kuchita zinthu zokhumudwitsa ena. Zimenezi ndi zosemphana ndi zimene munaphunzira, choncho muziwapewa.+