-
Aroma 16:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Koma tsopano chinsinsi chimenechi chaululidwa ndipo anthu a mitundu yonse achidziwa kudzera mʼMalemba aulosi. Zimenezi nʼzogwirizana ndi lamulo la Mulungu wamuyaya. Cholinga chake nʼchakuti anthu a mitundu yonse azimumvera mwa chikhulupiriro.
-