1 Akorinto 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi zinthu zamphamvu.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:27 Nsanja ya Olonda,6/15/2014, tsa. 248/15/1994, ptsa. 12-137/1/1988, ptsa. 28-29
27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi zinthu zamphamvu.+