2 Akorinto 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa zimene tikukulemberanizi ndi zinthu zoti mukhoza kuziwerenga* ndiponso kuzimvetsa. Ndipo ndikukhulupirira kuti mupitiriza kuzimvetsa bwino* zinthu zimenezi.
13 Chifukwa zimene tikukulemberanizi ndi zinthu zoti mukhoza kuziwerenga* ndiponso kuzimvetsa. Ndipo ndikukhulupirira kuti mupitiriza kuzimvetsa bwino* zinthu zimenezi.