2 Akorinto 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Popeza Mwana wa Mulungu, Yesu Khristu, amene ineyo, Silivano* ndi Timoteyo+ tinakulalikirani za iye, sanakhale “inde” kenako “ayi,” koma “inde” wakhalabe “inde.” 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,3/15/2014, tsa. 31
19 Popeza Mwana wa Mulungu, Yesu Khristu, amene ineyo, Silivano* ndi Timoteyo+ tinakulalikirani za iye, sanakhale “inde” kenako “ayi,” koma “inde” wakhalabe “inde.”