-
2 Akorinto 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndinalemba zimene zija kuti ndikadzabwera kumeneko, ndisadzakhale wachisoni chifukwa cha anthu amene ndiyenera kusangalala nawo. Chifukwa ndikukhulupirira kuti zimene zimandipangitsa kusangalala, zimapangitsanso nonsenu kusangalala.
-