2 Akorinto 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikuvutika, ndili ndi nkhawa kwambiri komanso ndikulira, osati kuti mumve chisoni,+ koma kuti mudziwe kuti ndimakukondani kwambiri. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda,11/1/1996, tsa. 11
4 Inetu ndinakulemberani kalata ija ndikuvutika, ndili ndi nkhawa kwambiri komanso ndikulira, osati kuti mumve chisoni,+ koma kuti mudziwe kuti ndimakukondani kwambiri.