2 Akorinto 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngati wina wachita zinthu zomvetsa chisoni,+ sanamvetse chisoni ineyo, koma kwenikweni wamvetsa chisoni nonsenu. Komabe sindikufuna kulankhula mwamphamvu za nkhani imeneyi.
5 Ngati wina wachita zinthu zomvetsa chisoni,+ sanamvetse chisoni ineyo, koma kwenikweni wamvetsa chisoni nonsenu. Komabe sindikufuna kulankhula mwamphamvu za nkhani imeneyi.