-
2 Akorinto 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Chifukwa kwa Mulungu ndife kafungo konunkhira bwino konena za uthenga wa Khristu, kamene kakumvedwa ndi anthu amene akukapulumutsidwa komanso amene akukawonongedwa.
-