2 Akorinto 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Malamulo amene amachititsa kuti munthu afe, amenenso analembedwa pamiyala,+ anabwera ndi ulemerero waukulu kwambiri moti Aisiraeli sanathe kuyangʼanitsitsa nkhope ya Mose chifukwa inkawala ndi ulemerero+ umene unatha patapita nthawi. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Nsanja ya Olonda,7/15/1990, tsa. 16
7 Malamulo amene amachititsa kuti munthu afe, amenenso analembedwa pamiyala,+ anabwera ndi ulemerero waukulu kwambiri moti Aisiraeli sanathe kuyangʼanitsitsa nkhope ya Mose chifukwa inkawala ndi ulemerero+ umene unatha patapita nthawi.