2 Akorinto 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngati malamulo olembedwa, amene anatha patapita nthawi, anaperekedwa ndi ulemerero,+ ndiye kuti malamulo amene sadzatha adzakhala ndi ulemerero waukulu kuposa pamenepo.+
11 Ngati malamulo olembedwa, amene anatha patapita nthawi, anaperekedwa ndi ulemerero,+ ndiye kuti malamulo amene sadzatha adzakhala ndi ulemerero waukulu kuposa pamenepo.+