2 Akorinto 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Timapanikizidwa mʼnjira zosiyanasiyana, koma osati mpaka kulephera kusuntha. Timathedwa nzeru, koma osati mpaka kusoweratu kothawira.*+
8 Timapanikizidwa mʼnjira zosiyanasiyana, koma osati mpaka kulephera kusuntha. Timathedwa nzeru, koma osati mpaka kusoweratu kothawira.*+