2 Akorinto 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ife tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi zimene zinalembedwa kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, choncho ndinalankhula.”+ Choncho ifenso tili ndi chikhulupiriro, ndipo tikulankhula,
13 Ife tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi zimene zinalembedwa kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, choncho ndinalankhula.”+ Choncho ifenso tili ndi chikhulupiriro, ndipo tikulankhula,