2 Akorinto 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene anatikonzekeretsa kuti tilandire zimenezi ndi Mulungu.+ Iye ndi amenenso anatipatsa mzimu kuti ukhale ngati chikole cha zinthu zamʼtsogolo.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2016, ptsa. 18-19 Nsanja ya Olonda,2/15/1998, tsa. 15
5 Amene anatikonzekeretsa kuti tilandire zimenezi ndi Mulungu.+ Iye ndi amenenso anatipatsa mzimu kuti ukhale ngati chikole cha zinthu zamʼtsogolo.+