2 Akorinto 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni tokha kwa inu. Koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira chifukwa cha ife, kuti muwayankhe amene amadzitama potengera maonekedwe akunja,+ osati zimene zili mumtima. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:12 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 16
12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni tokha kwa inu. Koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira chifukwa cha ife, kuti muwayankhe amene amadzitama potengera maonekedwe akunja,+ osati zimene zili mumtima.