2 Akorinto 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngati tinachita misala,+ tinachitira Mulungu. Koma ngati tili olongosoka, ndi zothandiza kwa inuyo. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 16
13 Ngati tinachita misala,+ tinachitira Mulungu. Koma ngati tili olongosoka, ndi zothandiza kwa inuyo.