2 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ngati osadziwika koma ndife odziwika bwino, ngati oti tikufa* koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa koma osaperekedwa kuti tikaphedwe,+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:9 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 20
9 ngati osadziwika koma ndife odziwika bwino, ngati oti tikufa* koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa koma osaperekedwa kuti tikaphedwe,+