-
2 Akorinto 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ponena zimenezi sikuti ndikukuimbani mlandu. Paja ndanena kale kuti inuyo muli mʼmitima yathu, kuti tife limodzi kapena tikhale ndi moyo limodzi.
-