2 Akorinto 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Titafika ku Makedoniya+ sitinapume koma tinapitiriza kukumana ndi mavuto osiyanasiyana. Anthu ena ankatitsutsa ndipo tinkadera nkhawa mipingo. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:5 Nsanja ya Olonda,6/15/2014, tsa. 2311/15/1998, tsa. 3011/1/1996, ptsa. 11-127/15/1992, tsa. 19
5 Titafika ku Makedoniya+ sitinapume koma tinapitiriza kukumana ndi mavuto osiyanasiyana. Anthu ena ankatitsutsa ndipo tinkadera nkhawa mipingo.