-
2 Akorinto 7:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma osati chifukwa tinali ndi Tito basi koma chifukwanso cha mmene inuyo munamulimbikitsira. Iye anatibweretseranso uthenga wakuti mukufunitsitsa kundiona, mukumva chisoni kwambiri ndiponso mukundidera nkhawa. Nditamva zimenezi ndinasangalalanso kwambiri.
-