2 Akorinto 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ngakhale kuti ndinakuchititsani kumva chisoni ndi kalata yanga,+ sindikudandaula. (Ndikuona kuti kalatayo inakuchititsani kumva chisoni, koma kwa nthawi yochepa.) Ndiye ngakhale kuti poyambapo ndinadandaula,
8 Choncho ngakhale kuti ndinakuchititsani kumva chisoni ndi kalata yanga,+ sindikudandaula. (Ndikuona kuti kalatayo inakuchititsani kumva chisoni, koma kwa nthawi yochepa.) Ndiye ngakhale kuti poyambapo ndinadandaula,