-
2 Akorinto 9:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho ndaona kuti ndi bwino kuti ndiuze abale kuti abwere kumeneko ife tisanafike, nʼcholinga choti adzakuthandizeni kukonzeratu mphatso imene munalonjeza kuti mudzapereka mowolowa manja. Zikatero, mphatsoyi idzakhala itakonzedwa kale ndipo zidzaonekeratu kuti mukuipereka mowolowa manja, osati mokakamizidwa.
-