2 Akorinto 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha umboni umene utumikiwu ukupereka, iwo akulemekeza Mulungu. Akutero chifukwa inuyo mwagonjera uthenga wabwino wonena za Khristu umene mukulengeza poyera ndiponso mwapereka mowolowa manja kwa iwowo ndi kwa anthu onse.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:13 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 210-212 Nsanja ya Olonda,10/15/1986, tsa. 23
13 Chifukwa cha umboni umene utumikiwu ukupereka, iwo akulemekeza Mulungu. Akutero chifukwa inuyo mwagonjera uthenga wabwino wonena za Khristu umene mukulengeza poyera ndiponso mwapereka mowolowa manja kwa iwowo ndi kwa anthu onse.+