2 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ambuye anatipatsa ulamuliro kuti tikulimbikitseni, osati kukufooketsani. Ndipo nditati ndidzitamandire mopitirirako malire zokhudza ulamulirowu,+ sindingachite manyazi.
8 Ambuye anatipatsa ulamuliro kuti tikulimbikitseni, osati kukufooketsani. Ndipo nditati ndidzitamandire mopitirirako malire zokhudza ulamulirowu,+ sindingachite manyazi.