2 Akorinto 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu amenewo adziwe kuti zimene tikunena mʼmakalata athu tili kwina, tidzachitanso zomwezo tikadzabwera.+
11 Anthu amenewo adziwe kuti zimene tikunena mʼmakalata athu tili kwina, tidzachitanso zomwezo tikadzabwera.+