2 Akorinto 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ifeyo sitidzadzitamandira pa zinthu zimene zili kunja kwa malire amene tapatsidwa. Tidzadzitamandira pa zinthu zimene zili mkati mwa malire a gawo limene Mulungu watiyezera, limene linafika mpaka kwanuko.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:13 Nsanja ya Olonda,7/15/2008, tsa. 28
13 Koma ifeyo sitidzadzitamandira pa zinthu zimene zili kunja kwa malire amene tapatsidwa. Tidzadzitamandira pa zinthu zimene zili mkati mwa malire a gawo limene Mulungu watiyezera, limene linafika mpaka kwanuko.+