2 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho sitikupitirira malire a gawo lathu, ngati kuti gawolo silikufika kwanuko. Chifukwa tinayamba ndife kufika kwanuko polengeza uthenga wabwino wonena za Khristu.+
14 Choncho sitikupitirira malire a gawo lathu, ngati kuti gawolo silikufika kwanuko. Chifukwa tinayamba ndife kufika kwanuko polengeza uthenga wabwino wonena za Khristu.+