-
2 Akorinto 10:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Sikutinso tikudzitamandira kunja kwa malire a gawo limene tinapatsidwa chifukwa cha ntchito ya munthu wina. Koma tikukhulupirira kuti chikhulupiriro chanu chikadzawonjezeka, ntchito yathunso idzakula mʼgawo lathu. Ndiyeno tidzakhala ndi zochita zambiri
-