-
2 Akorinto 11:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndikunena zimenezi modzinyoza tokha, popeza tikuoneka ngati tachita zinthu mofooka.
Koma ngati anthu ena akuchita zinthu molimba mtima, ndikulankhula ngati wopanda nzeru, inenso ndikuchita zinthu molimba mtima.
-