Agalatiya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikudabwa kuti mwapatuka mwamsanga* kuchoka kwa Mulungu amene anakuitanani kudzera mu kukoma mtima kwakukulu kwa Khristu ndipo mwayamba kumvetsera uthenga wabwino wamtundu wina.+
6 Ine ndikudabwa kuti mwapatuka mwamsanga* kuchoka kwa Mulungu amene anakuitanani kudzera mu kukoma mtima kwakukulu kwa Khristu ndipo mwayamba kumvetsera uthenga wabwino wamtundu wina.+