Agalatiya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa asanafike anthu ena ochokera kwa Yakobo,+ iye ankadya limodzi ndi anthu a mitundu ina.+ Koma anthuwo atafika, iye anasiya kuchita zimenezi ndipo anadzipatula, chifukwa ankaopa anthu odulidwawo.+
12 Chifukwa asanafike anthu ena ochokera kwa Yakobo,+ iye ankadya limodzi ndi anthu a mitundu ina.+ Koma anthuwo atafika, iye anasiya kuchita zimenezi ndipo anadzipatula, chifukwa ankaopa anthu odulidwawo.+