-
Agalatiya 2:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 tikudziwa kuti munthu amaonedwa kuti ndi wolungama, osati chifukwa chotsatira chilamulo, koma chifukwa chokhulupirira+ Yesu Khristu basi.+ Choncho ifeyo tikukhulupirira Khristu Yesu kuti tionedwe olungama chifukwa chokhulupirira Khristu, osati chifukwa chotsatira chilamulo. Tachita zimenezi chifukwa palibe munthu amene amaonedwa wolungama chifukwa chotsatira chilamulo.+
-