Agalatiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Sindikukana* kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ chifukwa ngati munthu amakhala wolungama potsatira chilamulo, ndiye kuti Khristu anangofa pachabe.+
21 Sindikukana* kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu,+ chifukwa ngati munthu amakhala wolungama potsatira chilamulo, ndiye kuti Khristu anangofa pachabe.+