Agalatiya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso, nʼzodziwikiratu kuti palibe munthu amene Mulungu angamuone kuti ndi wolungama chifukwa cha chilamulo,+ popeza “wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha chikhulupiriro chake.”+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Tsiku la Yehova, ptsa. 187-188
11 Komanso, nʼzodziwikiratu kuti palibe munthu amene Mulungu angamuone kuti ndi wolungama chifukwa cha chilamulo,+ popeza “wolungama adzakhala ndi moyo chifukwa cha chikhulupiriro chake.”+