-
Agalatiya 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Abale, ndipereke fanizo mogwirizana ndi zimene zimachitika pakati pa anthu: Pangano likakhazikitsidwa, ngakhale kuti ndi pangano la anthu, palibe amene angalithetse kapena kuwonjezerapo mfundo zina.
-