Agalatiya 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe chikhulupirirocho chisanafike, chilamulo ndi chimene chinkatiyangʼanira ndipo chinatiika mu ukapolo. Pa nthawi imeneyo, tinkayembekezera chikhulupiriro chimene chinali chitatsala pangʼono kuonekera.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:23 Nsanja ya Olonda,3/1/2008, tsa. 209/15/1991, ptsa. 12-13
23 Komabe chikhulupirirocho chisanafike, chilamulo ndi chimene chinkatiyangʼanira ndipo chinatiika mu ukapolo. Pa nthawi imeneyo, tinkayembekezera chikhulupiriro chimene chinali chitatsala pangʼono kuonekera.+