Agalatiya 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwachitsanzo, Malemba amanena kuti Abulahamu anabereka ana aamuna awiri, wina kwa kapolo wamkazi+ ndipo wina kwa mkazi amene anali mfulu.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:22 Nsanja ya Olonda,3/15/1992, tsa. 14
22 Mwachitsanzo, Malemba amanena kuti Abulahamu anabereka ana aamuna awiri, wina kwa kapolo wamkazi+ ndipo wina kwa mkazi amene anali mfulu.+